Ndipo Jonatani ndi Ahimaazi anakhala ku Enirogeli; mdzakazi adafopita kuwauza; ndipo iwo anapita nauza mfumu Davide, pakuti sangaoneke iwowo alikulowa m'mudzi.