Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 16:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inanena ndi Ziba, Ulikutani ndi zimenezi? Nati Ziba, Aburuwo ndiwo kuti akaberekepo a pa banja lanu; ndi mitanda ya mikate ndi zipatso za m'dzinja ndizo zakudya za anyamata; ndi vinyoyo akufoka m'cipululu akamweko.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:2 nkhani