Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 16:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pamene Davide anapitirira pang'ono pamutu pa phiri, onani, Ziba mnyamata wa Mefiboseti anakomana naye, ali nao aburu awiri omanga mbereko, ndi pamenepo mitanda ya mikate mazana awiri, ndi ncinci zamphesa zana limodzi, ndi zipatso za m'dzinja zana limodzi, ndi thumba la vinyo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 16

Onani 2 Samueli 16:1 nkhani