Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:31 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo wina anauza Davide nati, Ahitofeli ali pakati pa opangana ciwembu pamodzi ndi Abisalomu. Davide nati, Yehova, musandulize uphungu wa Ahitofeli ukhale wopusa.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:31 nkhani