Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anakwera pa cikweza ca ku Azitona nakwera nalira misozi; ndipo anapfunda mutu wace nayenda ndi mapazi osabvala; ndi anthu onse amene anali naye anapfunda munthu yense mutu wace, ndipo anakwera, nalira misozi pokwerapo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:30 nkhani