Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:32 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali pakufika Davide ku mutu wa phiri, kumene amapembedza Mulungu, onani, Husai M-ariki anadzakomana naye ali ndi maraya ace ong'ambika, ndi dothi pamutu pace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:32 nkhani