Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo dziko lonse linalira ndi mau okweza; ndipo anthu onse anaoloka, ndi mfumu yomwe inaoloka mtsinje wa Kidroni, ndipo anthu onse anaolokera ku njira ya kucipululu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:23 nkhani