Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:24 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo onani, Zadoki yemwe anadza, ndi Alevi onse pamodzi naye, alikunyamula likasa la cipangano la Mulungu; natula likasa la Mulungu; ndi Abyatara anakwera kufikira anthu onse anatha kuturuka m'mudzimo.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:24 nkhani