Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananena ndi Itai, Tiye nuoloke. Ndipo Itai Mgiti anaoloka, ndi anthu ace onse, ndi ana ang'ono onse amene anali naye.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:22 nkhani