Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abisalomu analawirira, nakaima pa njira ya kucipata; ndipo kunatero, pakakhala munthu ali yense ndi mrandu woyenera kufika kwa mfumu kuti aweruze, Abisalomu anamuitana, nati, Ndinu wa ku mudzi uti? Ndipo anati, Mnyamata wanu; ndiye wa pfuko tina la Aisrayeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:2 nkhani