Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 15:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, citapita ici Abisalomu anadzikonzera gareta ndi akavalo ndi anthu makumi asanu akuthamanga momtsogolera.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 15

Onani 2 Samueli 15:1 nkhani