Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 14:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mdzakazi wanu ndinati, Mau a mbuye wanga mfumu akhale opumulitsa; mbuye wanga mfumu ali ngati mthenga wa Mulungu, kuzindikira zabwino ndi zoipa; ndipo Yehova Mulungu wanu akhale nanu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 14

Onani 2 Samueli 14:17 nkhani