Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 11:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali pofikanso caka, nyengo yakuturuka mafumu, Davide anatumiza Yoabu, pamodzi ndi anyamata ace, ndi Aisrayeli onse; ndipo iwo anasakaza ana a Amoni, naumangira misasa yankhondo Raba. Koma Davide anatsaliraku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 11

Onani 2 Samueli 11:1 nkhani