Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 10:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide anati, Ndidzacitira Hanuni mwana wa Nahasi zokoma, monga atate wace anandicitira ine zokoma. Comweco Davide anatumiza ndi dzanja la anyamata ace kuti akamsangalatse cifukwa ca atate wace. Ndipo anyamata a Davide anafika ku dziko la ana a Amoni.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:2 nkhani