Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Samueli 10:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali zitapita izi, mfumu ya ana a Amoni inamwalira, ndipo Hanuni mwana wace anakhala mfumu m'malo mwace.

Werengani mutu wathunthu 2 Samueli 10

Onani 2 Samueli 10:1 nkhani