Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku lacisanu ndi citatu anacita msonkhano woletsa; popeza anacita zakupereka guwa la nsembe masiku asanu ndi awiri, ndi madyerero masiku asanu ndi awiri.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 7

Onani 2 Mbiri 7:9 nkhani