Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 7:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsiku la makumi awiri ndi citatu la mwezi wacisanu ndi ciwiri anawauza anthu apite ku mahema ao, akusekera ndi kukondwera m'mtima mwao cifukwa ca zokoma Yehova adawacitira Davide, ndi Solomo, ndi Aisrayeli anthu ace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 7

Onani 2 Mbiri 7:10 nkhani