Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 7:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Momwemo Solomo anatsiriza nyumba ya Yehova, ndi nyumba ya mfumu; ndipo ziri zonse zidalowa mumtima mwace mwa Solomo kuzicita m'nyumba ya Yehova, ndi m'nyumba yace yace, anacita mosabwezeza.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 7

Onani 2 Mbiri 7:11 nkhani