Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pemphero ndi pembedzero liri lonse likacitika ndi munthu ali yense, kapena ndi anthu anu onse Aisrayeli, akadziwa yense cinthenda cace, ndi cisoni cace, nakatambasulira manja ace kuloza ku nyumba iyi;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:29 nkhani