Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 6:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

pamenepo mumvere m'Mwamba mokhala Inumo, nimukhululukire, ndi kubwezera ali yense monga mwa njira zace zonse, monga mudziwa mtima wace; pakuti Inu, Inu nokha, mudziwa mitima ya ana a anthu;

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 6

Onani 2 Mbiri 6:30 nkhani