Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 36:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atero Koresi mfumu ya Perisiya, Yehova Mulungu Wam'mwamba anandipatsa maufumu onse a pa dziko lapansi, nandilangiza ndimmangire nyumba m'Yerusalemu, ndiwo ku Yuda. Ali yense mwa inu a anthu ace onse, Yehova Mulungu wace akhale naye, akwereko.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 36

Onani 2 Mbiri 36:23 nkhani