Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 36:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Caka coyamba tsono ca Koresi mfumu ya Perisiya, kuti akwaniridwe mau a Yehova pakamwa pa Yeremiya, Yehova anautsa mzimu wa Koresi mfumu ya Perisiya, kuti abukitse mau m'ufumu wace wonse, nawalembenso, ndi kuti,

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 36

Onani 2 Mbiri 36:22 nkhani