Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 34:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atakhala mfumu tsono zaka khumi mphambu zisanu ndi ziwiri, atayeretsa dziko ndi nyumbayi, anatuma safana mwana wa Azaliya, ndi Maseya kazembe wa mudzi, ndi Yona mwana wa Yoadazi wolemba mbiri, akonze nyumba ya Yehova Mulungu wace.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 34

Onani 2 Mbiri 34:8 nkhani