Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 29:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Hezekiya mfumu ndi akalonga anauzanso Alevi ayimbire Yehova zomlemekeza ndi mau a Davide ndi a Asafu mlauli. Ndipo anayimbira zomlemekeza mokondwera, nawerama mitu yao, nalambira.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 29

Onani 2 Mbiri 29:30 nkhani