Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 25:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi Yoasi mfumu ya Israyeli anatumiza kwa Amaziya mfumu ya Yuda ndi kuti, Mtungwi wa ku Lebano unatumiza kwa mkungudza wa ku Lebano, ndi kuti, Mpatse mwana wanga wamwamuna mwana wako wamkazi akhale mkazi wace; koma nyama ya kuthengo ya ku Lebano inapitapo, nipondereza mtungwi.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 25

Onani 2 Mbiri 25:18 nkhani