Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 18:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mthenga wakukaitana Mikaya ananena naye, ndi kuti, Taonani, mau a aneneri anenera mfumu cokoma ngati m'kamwa m'modzi; mau anu tsono akhaletu ngati amodzi a iwowa, nimunene cokoma.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 18

Onani 2 Mbiri 18:12 nkhani