Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 18:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndi aneneri onse ananenera momwemo, ndi kuti, Kwerani ku Ramoti Gileadi, mudzapindulako; pakuti Yehova adzaupereka m'dzanja la mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 18

Onani 2 Mbiri 18:11 nkhani