Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 14:14-15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

14. Ndipo anakantha midzi yonse pozungulira pace pa Gerari; a pakuti mantha ocokera kwa Yehova anawagwera; ndipo anafunkha m'midzi monse, pakuti mudacuruka zofunkha m'menemo.

15. Anakanthanso a m'mahema a ng'ombe, nalanda nkhosa zocuruka, ndi ngamila; nabwerera kumka ku Yerusalemu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 14