Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 14:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anakantha midzi yonse pozungulira pace pa Gerari; a pakuti mantha ocokera kwa Yehova anawagwera; ndipo anafunkha m'midzi monse, pakuti mudacuruka zofunkha m'menemo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 14

Onani 2 Mbiri 14:14 nkhani