Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mbiri 13:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo poceuka Yuda, taonani, nkhondo inayambana nao kumaso ndi kumbuyo; napfuulira iwo kwa Yehova, ndi ansembe analiza malipenga.

Werengani mutu wathunthu 2 Mbiri 13

Onani 2 Mbiri 13:14 nkhani