Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 8:27 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anayenda m'njira ya nyumba ya Ahabu, nacita coipa pamaso pa Yehova, m'mene inacitira nyumba ya Ahabu; pakuti ndiye wa cibale ca banja la Ahabu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:27 nkhani