Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 8:26 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ahaziya ndiye, Wa zaka makumi awiri mphambu ziwiri polowa ufumu wace, nakhala mfumu m'Yerusalemu caka cimodzi. Ndi dzina la mace ndiye Ataliya mdzukulu wa Omri mfumu ya Israyeli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 8

Onani 2 Mafumu 8:26 nkhani