Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 7:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo ananenana wina ndi mnzace, Sitirikucita bwino ife; tsiku lino ndilo tsiku la uthenga wabwino, ndipo tirikukhala cete; tikacedwa kufikira kwaca, mphulupulu yathu idzatipeza; tiyeni tsono, timuke, tifotokozere a m'nyumba ya mfumu.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:9 nkhani