Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 7:10 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nadza iwo, naitana mlonda wa mudzi, namfotokozera; ndi kuti, Tinafika ku misasa ya Aaramu, ndipo taonani, palibe munthu pomwepo, kapena mau a munthu, koma akavalo omanga, ndi aburu omanga, ndi mahema ali cimangire.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:10 nkhani