Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 7:8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pofika akhate ao polekezera pa misasa, analowa m'hema mmodzi, nadya namwa, natengako siliva ndi golidi ndi zobvala, namuka, nazibisa; nabwerera, nalowa m'hema mwina, natengako, namuka, nazibisa.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:8 nkhani