Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 7:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nayankha mmodzi wa anyamata ace, nati, Atenge tsono akavalo otsala asanu, ndiwo otsala m'mudzi; taonani, adzanga unyinji wonse wa Israyeli otsalawo, kapena adzanga unyinji wonse wa Israyeli otsirizika; tiwatumize tione.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:13 nkhani