Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 7:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Niuka mfumu usiku, ninena ndi anyamata ace, Ndikufotokozereni m'mene Aaramu aticitira ife. Adziwa kuti tagwidwa ndi njala, laturuka m'misasa, nabisala kuurengo, ndi kuti, Pamene aturuka m'mudzi tidzawagwira ndi moyo ndi kulowa m'mudzimo.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 7

Onani 2 Mafumu 7:12 nkhani