Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 5:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Potero anatsika, namira m'Yordano kasanu ndi kawiri, monga adanena munthu wa Mulunguyo; ndi mnofu wace unabwera monga mnofu wa mwana wamng'ono, nakonzeka.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:14 nkhani