Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 5:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo anyamata ace anasendera, nanena naye, nati, Atate wanga, mneneri akadakuuzani cinthu cacikuru, simukadacicita kodi? koposa kotani nanga ponena iye, Samba, nukonzeke?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 5

Onani 2 Mafumu 5:13 nkhani