Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:43 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mnyamata wace anati, Ciani? ndigawire amuna zana ici kodi? Koma anati, Uwapatse anthu kuti adye; pakuti atero Yehova, Adzadya nadzasivako.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:43 nkhani