Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 4:42 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anadza munthu kucokera ku Baala Salisa, nabwera nayo mikate ya zipatso zoyamba kwa munthu wa Mulungu, mikate ya barele makumi awiri, ndi ngala zaziwisi za tirigu zosaomba. Ndipo anati, Uwapatse anthu kuti adye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 4

Onani 2 Mafumu 4:42 nkhani