Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inalamulira Hilikiya mkulu wa ansembe, ndi ansembe a gawo laciwiri, ndi olindira pakhomo, aturutse m'Kacisi wa Yehova zipangizo adazipangira Baala, ndi cifanizo cija, ndi khamu lonse la kuthambo; nazitentha kunja kwa Yerusalemu ku thengo la ku Kidroni, natenga phulusa lace kumka nalo ku Beteli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:4 nkhani