Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Niima mfumu paciunda, nicita pangano pamaso pa Yehova, kutsata Yehova, ndi kusunga malamulo ace, ndi mboni zace, ndi malemba ace, ndi mtima wonse ndi moyo wonse, kukhazikitsa mau a cipangano colembedwa m'buku ili; ndipo anthu onse anaimiririra panganoli.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:3 nkhani