Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 23:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nikwera mfumu kumka ku nyumba ya Yehova, ndi amuna onse a Yuda, ndi onse okhala m'Yerusalemu pamodzi nave, ndi ansembe, ndi aneneri, ndi anthu onse ang'ono ndi akulu; nawerenga iye m'makutu mwao mau onse a m'buku la cipangano adalipeza m'nyumba ya Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 23

Onani 2 Mafumu 23:2 nkhani