Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 19:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Hezekiya analandira kalatayo ku dzanja la mithenga, namwerenga, nakwera Hezekiya kumka ku nyumba ya Yehova, namfunyulula pamaso pa Yehova.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 19

Onani 2 Mafumu 19:14 nkhani