Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mukati kwa ine, Tikhulupirira Yehova Mulungu wathu; sindiye amene Hezekiya wamcotsera misanje yace ndi maguwa a nsembe ace, nati kwa Yuda ndi kwa Yerusalemu, Muzilambira pa guwa la nsembe pane m'Yerusalemu?

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:22 nkhani