Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Taona tsono ukhulupirira ndodo ya bango ili lothyoka, ndilo Aigupto; ndilo munthu akatsamirapo lidzamlowa m'dzanja lace ndi kulibola; atero Farao mfumu ya Aigupto kwa onse omkhulupirira iye.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:21 nkhani