Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali caka cacitatu ca Hoseya mwana wa Ela mfumu ya Israyeli, Hezekiya mwana wa Ahazi mfumu ya Yuda analowa ufumu waceo

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:1 nkhani