Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 18:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndiye wa zaka makumi awiri ndi zisanu polowa ufumu wace, nakhala mfumu zaka makumi awiri mphambu zisanu ndi zinai m'Yerusalemu; ndi dzina la mace ndiye Abi mwana wa Zekariya.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 18

Onani 2 Mafumu 18:2 nkhani