Chipangano Chakale

Chipangano Chatsopano

2 Mafumu 10:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nawalembera kalata kaciwiri, nati, Mukakhala a ine ndi kumvera mau anga, tengani mitu va amunawo ana a mbuyewanu, ndi kundidzera ku Yezreeli mawa dzuwa lino. Koma ana a mfumu ndiwo amuna makumi asanu ndi awiri, anakhala ndi anthu omveka m'mudzi, amene anawalera.

Werengani mutu wathunthu 2 Mafumu 10

Onani 2 Mafumu 10:6 nkhani